Ezekieli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Iwe mwana wa munthu, kodi anthu opanduka a nyumba ya Isiraeli+ sanakufunse kuti, ‘Kodi ukuchita chiyani?’
9 “Iwe mwana wa munthu, kodi anthu opanduka a nyumba ya Isiraeli+ sanakufunse kuti, ‘Kodi ukuchita chiyani?’