Ezekieli 32:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Kumeneko kulinso dziko la Meseke,+ Tubala+ ndi makamu awo onse. Manda awo ali mozungulira mfumu yawo. Onsewa ndi anthu osadulidwa, anthu olasidwa ndi lupanga chifukwa chakuti anachititsa mantha anthu m’dziko la anthu amoyo.
26 “‘Kumeneko kulinso dziko la Meseke,+ Tubala+ ndi makamu awo onse. Manda awo ali mozungulira mfumu yawo. Onsewa ndi anthu osadulidwa, anthu olasidwa ndi lupanga chifukwa chakuti anachititsa mantha anthu m’dziko la anthu amoyo.