Ezekieli 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye anali kulakalaka kwambiri ana aamuna a ku Asuri.+ Anali kulakalaka abwanamkubwa ndi atsogoleri amene anali kukhala moyandikana naye. Amuna onsewa anali ovala mwaulemerero, asilikali okwera pamahatchi komanso anyamata osiririka.+
12 Iye anali kulakalaka kwambiri ana aamuna a ku Asuri.+ Anali kulakalaka abwanamkubwa ndi atsogoleri amene anali kukhala moyandikana naye. Amuna onsewa anali ovala mwaulemerero, asilikali okwera pamahatchi komanso anyamata osiririka.+