Ezekieli 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “Koma iwe mwana wa munthu, losera zokhudza mapiri a ku Isiraeli. Unene kuti, ‘Inu mapiri a ku Isiraeli,+ tamverani mawu a Yehova.
36 “Koma iwe mwana wa munthu, losera zokhudza mapiri a ku Isiraeli. Unene kuti, ‘Inu mapiri a ku Isiraeli,+ tamverani mawu a Yehova.