-
Ezekieli 40:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndiyeno ndinaona kuti panali nyumba yomwe inali ndi mpanda wozungulira nyumba yonseyo. M’manja mwa munthu uja munali bango loyezera. Bangolo linali lalitali kukwana mikono* 6 potengera muyezo wa mkono ndi chikhatho. Tsopano munthuyo anayamba kuyeza mpandawo, ndipo anapeza kuti unali wochindikala bango limodzi komanso kuchokera pansi kupita m’mwamba unali wautali bango limodzi.
-