-
Ezekieli 40:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Zipinda zake za alonda zinali zitatu mbali iyi ndiponso zitatu mbali inayo. Miyezo ya zipilala zake zam’mbali ndi khonde lake, inali yofanana ndi miyezo ya kanyumba ka pachipata choyamba chija. M’litali mwake kanali mikono 50 ndipo m’lifupi mwake kanali mikono 25.
-