-
Ezekieli 46:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Anthu a m’dzikoli akafika pamaso pa Yehova kuti adzam’gwadire ndi kumuweramira pa nyengo za chikondwerero,+ munthu amene walowa kudzera pachipata cha kumpoto+ azidzatulukira pachipata cha kum’mwera.+ Amene walowera pachipata cha kum’mwera azidzatulukira pachipata cha kumpoto. Munthu aliyense asadzatulukire pachipata chimene analowera. Aliyense azidzangoyenda kupita kutsogolo mpaka kukatuluka.
-