Levitiko 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nyama ya nsembe yopserezayo aziisenda chikopa ndi kuidula ziwaloziwalo.+ Levitiko 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atatero anaidula ziwaloziwalo,+ ndipo Mose anatenga mutu wake, ziwalozo ndi mafuta ake, ndi kuziika paguwa lansembe.
20 Atatero anaidula ziwaloziwalo,+ ndipo Mose anatenga mutu wake, ziwalozo ndi mafuta ake, ndi kuziika paguwa lansembe.