1 Mafumu 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Khomo lolowera+ kuchipinda cham’mbali chapansi linali kumanja kwa nyumbayo, ndipo ankakwera masitepe oyenda chokhotakhota kukafika kuchipinda chapakati. Kuchokera kuchipinda chimenechi, ankakwera n’kukafika kuchipinda chachitatu.
8 Khomo lolowera+ kuchipinda cham’mbali chapansi linali kumanja kwa nyumbayo, ndipo ankakwera masitepe oyenda chokhotakhota kukafika kuchipinda chapakati. Kuchokera kuchipinda chimenechi, ankakwera n’kukafika kuchipinda chachitatu.