Hoseya 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mtima wawo wakhala wachinyengo.+ Tsopano iwo adzapezeka ndi mlandu. “Pali wina amene adzathyola maguwa awo ansembe ndipo adzasakaza zipilala zawo zopatulika.+
2 Mtima wawo wakhala wachinyengo.+ Tsopano iwo adzapezeka ndi mlandu. “Pali wina amene adzathyola maguwa awo ansembe ndipo adzasakaza zipilala zawo zopatulika.+