Deuteronomo 32:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndikukweza dzanja langa kumwamba polumbira,+Ndipo ndikunena kuti: “Pali ine, Mulungu wamoyo wosatha,”+ Salimo 106:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho Mulungu anawalumbirira atakweza dzanja lake,+Kuti adzawapha m’chipululu,+
40 Ndikukweza dzanja langa kumwamba polumbira,+Ndipo ndikunena kuti: “Pali ine, Mulungu wamoyo wosatha,”+