1 Mafumu 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zitatero, mfumu inaika Benaya+ mwana wa Yehoyada m’malo mwa Yowabu kuti akhale mkulu wa asilikali,+ ndipo inaika wansembe Zadoki m’malo mwa Abiyatara.+
35 Zitatero, mfumu inaika Benaya+ mwana wa Yehoyada m’malo mwa Yowabu kuti akhale mkulu wa asilikali,+ ndipo inaika wansembe Zadoki m’malo mwa Abiyatara.+