Levitiko 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Ndipo aziphimba machimo a malo oyera chifukwa cha zodetsa+ za ana a Isiraeli ndi kusamvera kwawo m’machimo awo onse.+ Zimenezi azichitiranso chihema chokumanako chimene chili pakati pa ana a Isiraeli, amene ndi odetsedwa. Ezekieli 43:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kwa masiku 7, aphimbe machimo+ a guwalo ndipo aliyeretse ndi kuyamba kuligwiritsa ntchito.
16 “Ndipo aziphimba machimo a malo oyera chifukwa cha zodetsa+ za ana a Isiraeli ndi kusamvera kwawo m’machimo awo onse.+ Zimenezi azichitiranso chihema chokumanako chimene chili pakati pa ana a Isiraeli, amene ndi odetsedwa.