Levitiko 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndipo tchimo limene achitalo ladziwika,+ pamenepo mpingowo uzipereka ng’ombe yaing’ono yamphongo monga nsembe yamachimo, azibwera nayo pakhomo la chihema chokumanako.
14 ndipo tchimo limene achitalo ladziwika,+ pamenepo mpingowo uzipereka ng’ombe yaing’ono yamphongo monga nsembe yamachimo, azibwera nayo pakhomo la chihema chokumanako.