Ezekieli 47:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inuyo mutenge dera limeneli kuti likhale cholowa chanu. Limeneli likhale dziko la mafuko 12 a Isiraeli. Zigawo ziwiri zikhale za mbadwa za Yosefe.+
13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inuyo mutenge dera limeneli kuti likhale cholowa chanu. Limeneli likhale dziko la mafuko 12 a Isiraeli. Zigawo ziwiri zikhale za mbadwa za Yosefe.+