Ekisodo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+ Deuteronomo 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 chifaniziro cha chinthu chilichonse chimene chimayenda panthaka, ndi chifaniziro cha nsomba iliyonse+ ya m’madzi a pansi pa dziko.*
4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+
18 chifaniziro cha chinthu chilichonse chimene chimayenda panthaka, ndi chifaniziro cha nsomba iliyonse+ ya m’madzi a pansi pa dziko.*