Numeri 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mose ndi Aroni atamva zimenezi, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ pamaso pa khamu lonse la ana a Isiraeli. Numeri 16:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 “Amuna inu, chokani pakati pa khamuli kuti ndilifafanize kamodzi n’kamodzi.”+ Atamva zimenezi, iwo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+
5 Mose ndi Aroni atamva zimenezi, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ pamaso pa khamu lonse la ana a Isiraeli.
45 “Amuna inu, chokani pakati pa khamuli kuti ndilifafanize kamodzi n’kamodzi.”+ Atamva zimenezi, iwo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+