Ezekieli 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mawilowo anali kulowera kumbali zawo zonse zinayi. Akamayenda, sanali kukhota chifukwa chakuti anali kulowera kumene mitu ya akerubiwo* yayang’ana. Akamayenda sanali kukhota.+
11 Mawilowo anali kulowera kumbali zawo zonse zinayi. Akamayenda, sanali kukhota chifukwa chakuti anali kulowera kumene mitu ya akerubiwo* yayang’ana. Akamayenda sanali kukhota.+