Ezekieli 33:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Iwe mwana wa munthu, anthu okhala m’malo owonongedwa+ akulankhula za dziko la Isiraeli kuti, ‘Abulahamu anali munthu mmodzi koma anatenga dzikoli.+ Ife tilipo ambiri, choncho dzikoli laperekedwa kwa ife kuti likhale lathu.’+
24 “Iwe mwana wa munthu, anthu okhala m’malo owonongedwa+ akulankhula za dziko la Isiraeli kuti, ‘Abulahamu anali munthu mmodzi koma anatenga dzikoli.+ Ife tilipo ambiri, choncho dzikoli laperekedwa kwa ife kuti likhale lathu.’+