Yeremiya 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo+ kuwonongeka kwa anthu anga ponena kuti, ‘Kuli mtendere! Kuli mtendere!’ pamene kulibe mtendere.+ Yeremiya 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma mneneri amene walosera za mtendere+ amadziwika kuti ndi munthu amene Yehova wamutumadi ulosi wakewo ukakwaniritsidwa.”+
14 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo+ kuwonongeka kwa anthu anga ponena kuti, ‘Kuli mtendere! Kuli mtendere!’ pamene kulibe mtendere.+
9 Koma mneneri amene walosera za mtendere+ amadziwika kuti ndi munthu amene Yehova wamutumadi ulosi wakewo ukakwaniritsidwa.”+