Ezekieli 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Posachedwapa, ndikukhuthulirani ukali wanga,+ ndipo mkwiyo wanga ndiuthetsera pa inu.+ Ndikuweruzani mogwirizana ndi njira zanu,+ ndipo ndikubwezerani chifukwa cha zonyansa zanu zonse. Ezekieli 36:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo ndinawatsanulira mkwiyo wanga chifukwa cha magazi amene iwo anakhetsa m’dziko+ limenenso analidetsa ndi mafano awo onyansa.+
8 “‘Posachedwapa, ndikukhuthulirani ukali wanga,+ ndipo mkwiyo wanga ndiuthetsera pa inu.+ Ndikuweruzani mogwirizana ndi njira zanu,+ ndipo ndikubwezerani chifukwa cha zonyansa zanu zonse.
18 Pamenepo ndinawatsanulira mkwiyo wanga chifukwa cha magazi amene iwo anakhetsa m’dziko+ limenenso analidetsa ndi mafano awo onyansa.+