Mateyu 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma enawo anagwira akapolo akewo, ndi kuwachitira zachipongwe n’kuwapha.+