Yesaya 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 nsalu zovala kumutu, matcheni ovala kumiyendo, malamba a pachifuwa,+ zoikamo mafuta onunkhira,* zigoba zodzikongoletsera,+
20 nsalu zovala kumutu, matcheni ovala kumiyendo, malamba a pachifuwa,+ zoikamo mafuta onunkhira,* zigoba zodzikongoletsera,+