Yeremiya 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usachite mantha chifukwa cha nkhope zawo,+ pakuti Yehova wanena kuti, ‘Ine ndili ndi iwe kuti ndikulanditse.’”+
8 Usachite mantha chifukwa cha nkhope zawo,+ pakuti Yehova wanena kuti, ‘Ine ndili ndi iwe kuti ndikulanditse.’”+