Deuteronomo 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati munthuyo ndi wovutika, usagone ndi chinthu chake chimene wakupatsa monga chikolecho.+