Deuteronomo 28:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 “Yehova adzautsa mtundu wakutali, kumalekezero a dziko,+ mtundu umene chilankhulo chake sudzachimva.+ Mtunduwo udzakuukira monga mmene chiwombankhanga chimakhwathulira nyama yake,+ Yesaya 28:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti iye adzalankhula kwa anthu awa kudzera mwa anthu achibwibwi+ ndiponso olankhula lilime lachilendo,+
49 “Yehova adzautsa mtundu wakutali, kumalekezero a dziko,+ mtundu umene chilankhulo chake sudzachimva.+ Mtunduwo udzakuukira monga mmene chiwombankhanga chimakhwathulira nyama yake,+
11 Pakuti iye adzalankhula kwa anthu awa kudzera mwa anthu achibwibwi+ ndiponso olankhula lilime lachilendo,+