Yesaya 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu mukamabwerabwera kuti mudzaone nkhope yanga,+ kodi ndani wakuuzani kuti muchite zimenezi, kuti muzipondaponda mabwalo a panyumba panga?+
12 Inu mukamabwerabwera kuti mudzaone nkhope yanga,+ kodi ndani wakuuzani kuti muchite zimenezi, kuti muzipondaponda mabwalo a panyumba panga?+