Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ine ndidzakulowetsani m’dziko limene ndinalumbirira+ Abulahamu, Isaki ndi Yakobo, nditakweza dzanja langa. Ndidzakupatsani dzikolo kukhala lanu.+ Ine ndine Yehova.’”+

  • Deuteronomo 32:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ndikukweza dzanja langa kumwamba polumbira,+

      Ndipo ndikunena kuti: “Pali ine, Mulungu wamoyo wosatha,”+

  • Ezekieli 47:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Anthu inu muyenera kutenga dziko limeneli monga cholowa chanu. Inetu ndinalumbira nditakweza dzanja+ kuti ndidzapereka dziko limeneli kwa makolo anu.+ Choncho mugawane dzikoli mwa kuchita maere kuti likhale cholowa chanu. Aliyense alandire gawo lofanana ndi la m’bale wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena