Esitere 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 M’masiku a Ahasiwero,*+ amene anali kulamulira zigawo 127 monga mfumu, kuchokera ku Indiya mpaka ku Itiyopiya,+ Danieli 2:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Pa chifukwa chimenechi, mfumu inamukweza pa udindo Danieli+ ndipo inamupatsa mphatso zambiri. Inamuikanso kukhala wolamulira chigawo chonse cha Babulo+ ndiponso wamkulu wa akuluakulu a boma* oyang’anira amuna onse anzeru a m’Babulo.
1 M’masiku a Ahasiwero,*+ amene anali kulamulira zigawo 127 monga mfumu, kuchokera ku Indiya mpaka ku Itiyopiya,+
48 Pa chifukwa chimenechi, mfumu inamukweza pa udindo Danieli+ ndipo inamupatsa mphatso zambiri. Inamuikanso kukhala wolamulira chigawo chonse cha Babulo+ ndiponso wamkulu wa akuluakulu a boma* oyang’anira amuna onse anzeru a m’Babulo.