Ekisodo 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.+ Mateyu 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako anamuuza kuti: “Ndikupatsani zinthu zonsezi+ ngati mutangogwada pansi n’kundiweramira kamodzi kokha.”+
5 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.+
9 Kenako anamuuza kuti: “Ndikupatsani zinthu zonsezi+ ngati mutangogwada pansi n’kundiweramira kamodzi kokha.”+