Miyambo 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wokonda kukwiya amayambitsa mkangano,+ ndipo aliyense wokonda kupsa mtima amakhala ndi machimo ambiri.+ Danieli 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mfumu itamva zimenezi inapsa mtima ndipo inakwiya kwambiri,+ moti inanena kuti amuna onse anzeru a m’Babulo ayenera kuphedwa.+
22 Munthu wokonda kukwiya amayambitsa mkangano,+ ndipo aliyense wokonda kupsa mtima amakhala ndi machimo ambiri.+
12 Mfumu itamva zimenezi inapsa mtima ndipo inakwiya kwambiri,+ moti inanena kuti amuna onse anzeru a m’Babulo ayenera kuphedwa.+