Yesaya 47:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Alangizi ako ambirimbiri akutopetsa. Anthu opembedza zinthu zakumwamba, oyang’anitsitsa kayendedwe ka nyenyezi,+ amene amalosera zimene zichitike kwa iwe mwezi watsopano ukakhala, tsopano aimirire ndi kukupulumutsa. Danieli 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Danieli anayankha mfumuyo kuti: “Chinsinsi chimene inu mfumu mukufuna kudziwa, amuna anzeru, anthu olankhula ndi mizimu, ansembe ochita zamatsenga ndi anthu okhulupirira nyenyezi, alephera kukuuzani.+
13 Alangizi ako ambirimbiri akutopetsa. Anthu opembedza zinthu zakumwamba, oyang’anitsitsa kayendedwe ka nyenyezi,+ amene amalosera zimene zichitike kwa iwe mwezi watsopano ukakhala, tsopano aimirire ndi kukupulumutsa.
27 Danieli anayankha mfumuyo kuti: “Chinsinsi chimene inu mfumu mukufuna kudziwa, amuna anzeru, anthu olankhula ndi mizimu, ansembe ochita zamatsenga ndi anthu okhulupirira nyenyezi, alephera kukuuzani.+