Danieli 2:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 inuyo amene Mulungu wakupatsani+ nyama zakutchire ndi mbalame zam’mlengalenga kulikonse kumene kuli anthu, amene Mulungu wakuikani kukhala wolamulira zonsezo, inuyo ndiye mutu wagolide.+
38 inuyo amene Mulungu wakupatsani+ nyama zakutchire ndi mbalame zam’mlengalenga kulikonse kumene kuli anthu, amene Mulungu wakuikani kukhala wolamulira zonsezo, inuyo ndiye mutu wagolide.+