Genesis 41:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kutacha m’mawa, Farao anavutika kwambiri ndi maganizo.+ Chotero anaitanitsa ansembe onse amatsenga+ ndi amuna anzeru+ onse a mu Iguputo, n’kuwafotokozera maloto akewo.+ Koma palibe amene anatha kum’masulira Farao malotowo. Danieli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo mfumuyo inalamula kuti aitane ansembe onse ochita zamatsenga,+ anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi anthu ena ochita zamatsenga kuti adzauze mfumu maloto akewo.+ Anthu amenewa anafika ndi kuima pamaso pa mfumu. Danieli 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo ndinalamula kuti amuna onse anzeru a m’Babulo abwere kwa ine kuti adzandimasulire malotowo.+
8 Kutacha m’mawa, Farao anavutika kwambiri ndi maganizo.+ Chotero anaitanitsa ansembe onse amatsenga+ ndi amuna anzeru+ onse a mu Iguputo, n’kuwafotokozera maloto akewo.+ Koma palibe amene anatha kum’masulira Farao malotowo.
2 Pamenepo mfumuyo inalamula kuti aitane ansembe onse ochita zamatsenga,+ anthu olankhula ndi mizimu, Akasidi* ndi anthu ena ochita zamatsenga kuti adzauze mfumu maloto akewo.+ Anthu amenewa anafika ndi kuima pamaso pa mfumu.
6 Pamenepo ndinalamula kuti amuna onse anzeru a m’Babulo abwere kwa ine kuti adzandimasulire malotowo.+