Danieli 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Inuyo mfumu, mfumu ya mafumu, inu amene Mulungu wakumwamba wakupatsani ufumu,+ mphamvu, ndi ulemerero, Danieli 2:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 inuyo amene Mulungu wakupatsani+ nyama zakutchire ndi mbalame zam’mlengalenga kulikonse kumene kuli anthu, amene Mulungu wakuikani kukhala wolamulira zonsezo, inuyo ndiye mutu wagolide.+
37 Inuyo mfumu, mfumu ya mafumu, inu amene Mulungu wakumwamba wakupatsani ufumu,+ mphamvu, ndi ulemerero,
38 inuyo amene Mulungu wakupatsani+ nyama zakutchire ndi mbalame zam’mlengalenga kulikonse kumene kuli anthu, amene Mulungu wakuikani kukhala wolamulira zonsezo, inuyo ndiye mutu wagolide.+