2 Samueli 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,+Ndinaitana Mulungu wanga.+Pamenepo iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake,+Makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+ Salimo 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ine chikhulupiriro changa chili mwa inu Yehova.+Ndipo ndikunena kuti: “Inu ndinu Mulungu wanga.”+
7 Pa nthawi ya zowawa zanga ndinaitana Yehova,+Ndinaitana Mulungu wanga.+Pamenepo iye anamva mawu anga ali m’kachisi wake,+Makutu ake anamva kulira kwanga kopempha thandizo.+
14 Koma ine chikhulupiriro changa chili mwa inu Yehova.+Ndipo ndikunena kuti: “Inu ndinu Mulungu wanga.”+