Danieli 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako ndinamva mawu a munthu wochokera kufumbi ali pakati pa mtsinje wa Ulai.+ Iye anafuula kuti: “Gabirieli,+ thandiza uyo ali apoyo kuti amvetsetse zimene waona.”+
16 Kenako ndinamva mawu a munthu wochokera kufumbi ali pakati pa mtsinje wa Ulai.+ Iye anafuula kuti: “Gabirieli,+ thandiza uyo ali apoyo kuti amvetsetse zimene waona.”+