Danieli 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 ndipo Dariyo+ Mmedi anapatsidwa ufumuwo ali ndi zaka pafupifupi 62. Danieli 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Dariyo anaona kuti ndi bwino kuti aike masatarapi* 120 oyang’anira zigawo zonse za ufumu wake.+ Danieli 6:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho zinthu zinamuyendera bwino Danieli mu ufumu wa Dariyo+ ndiponso mu ufumu wa Koresi Mperisiya.+
6 Ndiyeno Dariyo anaona kuti ndi bwino kuti aike masatarapi* 120 oyang’anira zigawo zonse za ufumu wake.+
28 Choncho zinthu zinamuyendera bwino Danieli mu ufumu wa Dariyo+ ndiponso mu ufumu wa Koresi Mperisiya.+