Genesis 41:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo Yosefe anayankha Farao kuti: “Yemwe anene uthenga wokhudza moyo wa inu Farao ndi Mulungu osati ine.”+
16 Pamenepo Yosefe anayankha Farao kuti: “Yemwe anene uthenga wokhudza moyo wa inu Farao ndi Mulungu osati ine.”+