Danieli 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wa mfumu Belisazara,+ ineyo Danieli ndinaona masomphenya pambuyo pa masomphenya amene ndinaona poyambirira aja.+
8 M’chaka chachitatu cha ulamuliro wa mfumu Belisazara,+ ineyo Danieli ndinaona masomphenya pambuyo pa masomphenya amene ndinaona poyambirira aja.+