Luka 19:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Chifukwa masiku adzakufikira pamene adani ako adzamanga mpanda+ wazisonga+ kukuzungulira.+ Adaniwo adzakutsekereza ndi kukusautsa+ kuchokera kumbali zonse. Luka 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Chinanso, mukadzaona magulu ankhondo atazungulira Yerusalemu,+ mudzadziwe kuti chiwonongeko chake chayandikira.+
43 Chifukwa masiku adzakufikira pamene adani ako adzamanga mpanda+ wazisonga+ kukuzungulira.+ Adaniwo adzakutsekereza ndi kukusautsa+ kuchokera kumbali zonse.
20 “Chinanso, mukadzaona magulu ankhondo atazungulira Yerusalemu,+ mudzadziwe kuti chiwonongeko chake chayandikira.+