Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Kenako ndinaonanso m’masomphenya ausiku chilombo chachinayi, choopsa kwambiri ndiponso chochititsa mantha komanso champhamvu kwambiri.+ Chinali ndi mano akuluakulu achitsulo ndipo chinali kudya ndi kuphwanyaphwanya chilichonse chimene chinali nacho pafupi. Zotsala chinali kuzipondaponda ndi mapazi ake. Chinali chosiyana ndi zilombo zina zonse zimene ndinaona poyamba ndipo chinali ndi nyanga 10.+

  • Danieli 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “Ndiyeno iye anandiuza kuti, ‘Ponena za chilombo chachinayi chimenechi, pali ufumu wachinayi umene udzakhalapo padziko lapansi. Udzakhala wosiyana ndi maufumu ena onse. Udzadya dziko lonse lapansi ndipo udzalipondaponda ndi kuliphwanyaphwanya.+

  • Luka 21:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Chinanso, mukadzaona magulu ankhondo atazungulira Yerusalemu,+ mudzadziwe kuti chiwonongeko chake chayandikira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena