Ezara 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso, anali kulemba ntchito+ aphungu kuti alepheretse zolinga zawo masiku onse a Koresi mfumu ya Perisiya, mpaka ulamuliro wa Dariyo+ mfumu ya Perisiya.
5 Komanso, anali kulemba ntchito+ aphungu kuti alepheretse zolinga zawo masiku onse a Koresi mfumu ya Perisiya, mpaka ulamuliro wa Dariyo+ mfumu ya Perisiya.