Ezara 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mu ulamuliro wa Ahasiwero, kumayambiriro kwa ulamuliro wake, iwo analemba kalata yoneneza+ anthu okhala ku Yuda ndi ku Yerusalemu.
6 Mu ulamuliro wa Ahasiwero, kumayambiriro kwa ulamuliro wake, iwo analemba kalata yoneneza+ anthu okhala ku Yuda ndi ku Yerusalemu.