-
Danieli 11:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 “Ndiyeno patatha zaka zingapo iwo adzagwirizana, ndipo mwana wamkazi wa mfumu ya kum’mwera adzapita kwa mfumu ya kumpoto kuti apange mgwirizano. Koma mwana wamkaziyo sadzakhala ndi mphamvu m’dzanja lake,+ ndipo mfumuyo sidzalimba, ngakhalenso dzanja lake silidzalimba. Mwana wamkaziyo adzaperekedwa m’manja mwa anthu ena, pamodzi ndi amene anamubweretsa, amene anamubereka ndiponso amene anamuchititsa kukhala wamphamvu masiku amenewo.
-