1 Akorinto 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Sizingatheke kuti muzimwa za m’kapu ya Yehova*+ komanso za m’kapu ya ziwanda. Sizingatheke kuti muzidya “patebulo la Yehova”+ komanso patebulo la ziwanda. 1 Timoteyo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+
21 Sizingatheke kuti muzimwa za m’kapu ya Yehova*+ komanso za m’kapu ya ziwanda. Sizingatheke kuti muzidya “patebulo la Yehova”+ komanso patebulo la ziwanda.
4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+