Danieli 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anafunsa Arioki mkulu wa asilikali olondera mfumu uja kuti: “Chavuta n’chiyani kuti mfumu ipereke lamulo lokhwima chonchi?” Pamenepo, Arioki anafotokoza nkhani yonse ija kwa Danieli.+
15 Iye anafunsa Arioki mkulu wa asilikali olondera mfumu uja kuti: “Chavuta n’chiyani kuti mfumu ipereke lamulo lokhwima chonchi?” Pamenepo, Arioki anafotokoza nkhani yonse ija kwa Danieli.+