Zekariya 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako ndinachotsa abusa atatu m’mwezi umodzi+ chifukwa sindinathenso kuleza nawo mtima,+ ndipo iwonso ananyansidwa nane.
8 Kenako ndinachotsa abusa atatu m’mwezi umodzi+ chifukwa sindinathenso kuleza nawo mtima,+ ndipo iwonso ananyansidwa nane.