Hoseya 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wina adzapititsa fanolo kudziko la Asuri ndi kukalipereka monga mphatso kwa mfumu yaikulu.+ Efuraimu adzachita manyazi+ ndipo Isiraeli adzachita manyazi ndi zoipa zimene anali kufuna kuchita.+
6 Wina adzapititsa fanolo kudziko la Asuri ndi kukalipereka monga mphatso kwa mfumu yaikulu.+ Efuraimu adzachita manyazi+ ndipo Isiraeli adzachita manyazi ndi zoipa zimene anali kufuna kuchita.+