Hoseya 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo adzabwera akunjenjemera ngati mbalame kuchokera ku Iguputo.+ Adzabweranso akunjenjemera ngati njiwa kuchokera kudziko la Asuri+ ndipo ndidzawachititsa kukhala m’nyumba zawo,” watero Yehova.+
11 Iwo adzabwera akunjenjemera ngati mbalame kuchokera ku Iguputo.+ Adzabweranso akunjenjemera ngati njiwa kuchokera kudziko la Asuri+ ndipo ndidzawachititsa kukhala m’nyumba zawo,” watero Yehova.+